Mlaliki 2:21 BL92

21 Pakuti pali munthu wina agwira nchito mwanzeru ndi modziwa nadzipinduliramo; koma adzapereka gawo lace kwa munthu amene sanagwirapo nchito. Icinso ndi cabe ndi coipa cacikuru.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 2

Onani Mlaliki 2:21 nkhani