Mlaliki 2:8 BL92

8 ndinakundikanso siliva ndi golidi ndi cuma ca mafumu ndi madera a dziko; ndinaitanitsa amuna ndi akazi akuyimba ndi zokondweretsazo za ana a anthu, ndizo zoyimbira za mitundu mitundu.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 2

Onani Mlaliki 2:8 nkhani