11 Cinthu ciri conse anacikongoletsa pa mphindi yace; ndipo waika zamuyaya m'mitima yao ndipo palibe munthu angalondetse nchito Mulungu wazipanga ciyambire mpaka citsiriziro.
Werengani mutu wathunthu Mlaliki 3
Onani Mlaliki 3:11 nkhani