14 Ndidziwa kuti zonse Mulungu azicita zidzakhala kufikira nthawi zonse; sungaonjezepo kanthu, ngakhale kucotsapo; Mulungu nazicita kuti anthu akaope pamaso pace.
Werengani mutu wathunthu Mlaliki 3
Onani Mlaliki 3:14 nkhani