Mlaliki 3:19 BL92

19 Pakuti comwe cigwera ana a anthu cigweranso nyamazo; ngakhale cowagwera ncimodzimodzi; monga winayo angofa momwemo zinazo zifanso; inde onsewo ali ndi mpweya umodzi; ndipo munthu sapambana nyama pakuti zonse ndi cabe,

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 3

Onani Mlaliki 3:19 nkhani