Mlaliki 4:15 BL92

15 Ndinapenyera anthu onse amoyo akuyenda kunja kuno, kuti anali ndi mwana, waciwiri, amene adzalowa m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 4

Onani Mlaliki 4:15 nkhani