Mlaliki 5:10 BL92

10 Wokonda siliva sadzakhuta siliva; ngakhale wokonda cuma sadzakhuta phindu; icinso ndi cabe.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 5

Onani Mlaliki 5:10 nkhani