Mlaliki 5:13 BL92

13 Pali coipa cobvuta ndaciona kunja kuno, ndico, cuma cirikupweteka eni ace pocikundika;

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 5

Onani Mlaliki 5:13 nkhani