Mlaliki 5:20 BL92

20 Pakuti sadzakumbukira masiku a moyo wace kwambiri; cifukwa Mulungu ambvomereza m'cimwemwe ca mtima wace.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 5

Onani Mlaliki 5:20 nkhani