Mlaliki 5:6 BL92

6 Usalole m'kamwa mwako mucimwitse thupi lako; usanene pamaso pa mthenga kuti, Ndinaphophonya; Mulungu akwiyire mau ako cifukwa ninji, naononge nchito ya manja ako?

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 5

Onani Mlaliki 5:6 nkhani