Mlaliki 5:8 BL92

8 Ukaona anthu alikutsendereza aumphawi, ndi kucotsa cilungamo ndi ciweruzo mwaciwawa pa dera lina la dziko, usazizwepo; pakuti mkuru wopambana asamalira; ndipo alipo akuru ena oposa amenewo.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 5

Onani Mlaliki 5:8 nkhani