Mlaliki 7:9 BL92

9 Usakangaze mumtima mwako kukwiya; pakuti mkwiyo ugona m'cifuwa ca zitsiru.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 7

Onani Mlaliki 7:9 nkhani