Mlaliki 8:1 BL92

1 Ndani akunga wanzeru? Ndani adziwa tanthauzo la mau? Nzeru ya munthu iwalitsa nkhope yace, kuduwa kwa nkhope yace ndi kusanduka.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 8

Onani Mlaliki 8:1 nkhani