13 koma woipa sadzapeza bwino ngakhale kutanimphitsa masiku ace ngati mthunzi; cifukwa saopa pamaso pa Mulungu.
Werengani mutu wathunthu Mlaliki 8
Onani Mlaliki 8:13 nkhani