17 Pfuulanso, ndi kuti, Atero Yehova wa makamu: Midzi yanga idzalemerera ndi kufalikiranso; ndipo Yehova adzasangalatsanso Ziyoni, nadzasankhamo Yerusalemu.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 1
Onani Zekariya 1:17 nkhani