3 Cifukwa cace uziti nao, Atero Yehova wa makamu: Bwererani kudza kwa Ine, ati Yehova wa makamu, ndipo Ine ndidzabwerera kudza kwa inu, ati Yehova wa makamu.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 1
Onani Zekariya 1:3 nkhani