Zekariya 10:10 BL92

10 Ndidzawatenganso ku dziko la Aigupto, ndi kuwasonkhanitsa m'Asuri; ndipo ndidzalowa nao m'dziko la Gileadi ndi Lebano; koma sadzawafikira.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 10

Onani Zekariya 10:10 nkhani