Zekariya 10:5 BL92

5 Ndipo adzakhala ngati ngwazi zakupondereza adani m'thope la kubwalo kunkhondo; ndipo adzacita nkhondo, cifukwa Yehova ali nao; ndi apakavalo adzacitidwa manyazi.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 10

Onani Zekariya 10:5 nkhani