Zekariya 10:7 BL92

7 Ndipo iwo a ku Efraimu adzakhala ngati ngwazi, ndi mtima wao udzakondwera ngati ndi vinyo; ndipo ana ao adzaciona nadzakondwera; mtima wao udzakondwerera mwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 10

Onani Zekariya 10:7 nkhani