10 Ndipo ndinatenga ndodo yanga Cisomo, ndi kuidula pakati, kuti ndiphwanye pangano langa ndinalicita ndi mitundu yonse ya anthu.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 11
Onani Zekariya 11:10 nkhani