7 Ndipo Yehova adzayamba kupulumutsa mahema a Yuda, kuti ulemerero wa nyumba ya Davide ndi ulemerero wa okhala m'Yerusalemu usakulire Yuda.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 12
Onani Zekariya 12:7 nkhani