3 Pamenepo Yehova adzaturuka, nadzacita nkhondo ndi amitundu aja, monga anacitira nkhondo tsiku lakudumana.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 14
Onani Zekariya 14:3 nkhani