7 koma lidzakhala tsiku la pa lokha lodziwika ndi Yehova; palibe usana, palibe usiku; koma kudzatero kuti madzulo kudzati mbe.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 14
Onani Zekariya 14:7 nkhani