Zekariya 2:11 BL92

11 Ndipo amitundu ambiri adzaphatikidwa kwa Yehova tsiku ilo, nadzakhala anthu anga; ndipo ndidzakhala pakati pako, ndipo udzadziwa kuti Yehova wa makamu anandituma kwa iwe.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 2

Onani Zekariya 2:11 nkhani