Zekariya 2:2 BL92

2 Ndipo ndinati, Upita kuti? Ndipo anati kwa ine, Kukayesa Yerusalemu, kuona ngati citando cace ncotani, ndi m'litali mwace motani.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 2

Onani Zekariya 2:2 nkhani