Zekariya 3:1 BL92

1 Pamenepo anandionetsa Yoswa mkulu wa ansembe alikuima pamaso pa mthenga wa Yehova, ndi Satana alikuima pa dzanja lace lamanja, atsutsana naye.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 3

Onani Zekariya 3:1 nkhani