Zekariya 3:10 BL92

10 Tsiku lomwelo, ati Yehova wa makamu, mudzaitanizana yense mnansi wace patsinde pa mpesa ndi patsinde pa mkuyu.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 3

Onani Zekariya 3:10 nkhani