5 Ndipo ndinati, Amuike nduwira yoyera pamutu pace. Naika nduwira yoyera pamutu pace, nambveka ndi zobvala; ndi mthenga wa Yehova anaimirirapo,
Werengani mutu wathunthu Zekariya 3
Onani Zekariya 3:5 nkhani