Zekariya 4:7 BL92

7 Ndiwe yani, phiri lalikuru iwe? pamaso pa Zerubabele udzasanduka cidikha; ndipo adzaturutsa mwala wa cimbudzi, ndi kupfuula, Cisomo, cisomo nao.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 4

Onani Zekariya 4:7 nkhani