Zekariya 4:9 BL92

9 Manja a Zerubabele anaika maziko a nyumba iyi, manja ace omwe adzaitsiriza; ndipo udzadziwa kuti Yehova wa makatnu anandituma kwa inu.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 4

Onani Zekariya 4:9 nkhani