Zekariya 5:2 BL92

2 Ndipo anati kwa ine, Uona ciani? Ndipo ndinayankha, Ndiona mpukutu wouluka; utali wace mikono makumi awiri, ndi citando cace mikono khumi.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 5

Onani Zekariya 5:2 nkhani