Zekariya 5:5 BL92

5 Pamenepo mthenga wakulankhula ndi ine anaturuka, nati kwa ine, Kwezatu maso ako, nuone ngati nciani ici cirikuturukaci.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 5

Onani Zekariya 5:5 nkhani