Zekariya 6:10 BL92

10 Tenga a iwo a kundende, a Keledai, a Tobiya, ndi a Yedaya; nudze tsiku lomwelo, nulowe ku nyumba ya Yosiya, mwana wa Zefaniya, kumene anafikirako kucokera ku Babulo,

Werengani mutu wathunthu Zekariya 6

Onani Zekariya 6:10 nkhani