Zekariya 6:8 BL92

8 Ndipo anandiitana, nanena nane, kuti, Taonani, iwo akuturuka kumka ku dziko la kumpoto anapumulitsa Mzimu wanga m'dziko lakumpoto.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 6

Onani Zekariya 6:8 nkhani