14 Ndipo Yehova adzaoneka pamwamba pao, ndi mubvi wace udzaturuka ngati mphezi; ndipo Ambuye Mulungu adzaomba lipenga, nadzayenda ndi akabvumvulu a kumwela.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 9
Onani Zekariya 9:14 nkhani