Zekariya 9:16 BL92

16 Ndipo Yehova Mulungu wao adzawapulumutsa tsiku ilo, ngati zoweta za anthu ace; pakuti adzakhala ngati miyala ya m'korona yakunyezimira pa dziko lace.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 9

Onani Zekariya 9:16 nkhani