Zekariya 9:3 BL92

3 Ndipo Turo adzadzimangira polimbikirapo, nadzakundika siliva ngati pfumbi, ndi golidi woyenga ngati thope la kubwalo.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 9

Onani Zekariya 9:3 nkhani