Ahebri 12:27 BL92

27 Ndipo ici, cakuti kamodzinso, cilozera kusuntha kwace kwa zinthu zogwedezeka, monga kwa zinthu zolengedwa, kuti zinthu zosagwedezeka zikhale.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 12

Onani Ahebri 12:27 nkhani