28 Mwa ici polandira ufumu wosagwedezeka, tikhale naco cisomo, cimene tikatumikire naco Mulungu momkondweretsa, ndi kumcitira ulemu ndi mantha.
Werengani mutu wathunthu Ahebri 12
Onani Ahebri 12:28 nkhani