Ahebri 13:23 BL92

23 Zindikirani kuti mbale wathu 4 Timoteo wamasulidwa; pamodzi ndi iye, ngati akudza msanga, ndidzakuonani inu.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 13

Onani Ahebri 13:23 nkhani