10 Pakuti iye amene adalowa mpumulo wace, adapumulanso mwini wace ku nchito zace, monganso Mulungu ku zace za iye.
Werengani mutu wathunthu Ahebri 4
Onani Ahebri 4:10 nkhani