28 Pakuti cilamulo cimaika akuru a ansembe anthu, okhala naco cifoko; koma mau a lumbirolo, amene anafika citapita cilamulo, aika Mwana, woyesedwa wopanda cirema ku nthawi zonse.
Werengani mutu wathunthu Ahebri 7
Onani Ahebri 7:28 nkhani