Ahebri 8:1 BL92

1 Koma mutu wafzi tanenazi ndi uwu: Tiri naye Mkuruwansembe wotere, amene anakhala pa dzanja lamanja la mpando wacifumu wa Ukulu m'Kumwamba,

Werengani mutu wathunthu Ahebri 8

Onani Ahebri 8:1 nkhani