1 Tamverani mau awa, inu ng'ombe zazikazi za ku Basana, zokhala m'phiri la Samariya, zosautsa aumphawi, zopsinja osowa, zonena kwa ambuyao, Bwerani naco, timwe.
Werengani mutu wathunthu Amosi 4
Onani Amosi 4:1 nkhani