Zekariya 1:11 BL92

11 Ndipo iwo anamyankha mthenga wa Yehova wakuima pakati pa mitengo yamcisu, nati, Tayendayenda m'dziko, ndipo taonani, dziko lonse likhala cete, lipumula.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 1

Onani Zekariya 1:11 nkhani