Zekariya 1:14 BL92

14 Ndipo mthenga wakulankhula ndi ine anati kwa ine, Pfuula, ndi kuti, Atero Yehova wa makamu: Ndicitira nsanje Yerusalemu ndi Ziyoni ndi nsanje yaikuru.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 1

Onani Zekariya 1:14 nkhani