8 Ndinaona usiku, taonani, munthu woyenda pa kavalo wofiira, alikuima pakati pa mitengo yamcisu inali kunsi; ndi pambuyo pace panali akavalo ofiira, odera ndi oyera.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 1
Onani Zekariya 1:8 nkhani