Zekariya 1:9 BL92

9 Pamenepo ndinati, Awa ndi ciani, mbuyanga? Ndi mthenga wakulankhula ndi ine anati kwa ine, Ndidzakuonetsa awa ndi ciani.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 1

Onani Zekariya 1:9 nkhani