Zekariya 10:3 BL92

3 Mkwiyo wanga wayakira abusa, ndipo ndidzalanga atonde; pakuti Yehova wa makamu adzazonda zoweta zace, ndizo nyumba ya Yuda, nadzaziika ngati kavalo wace waulemerero kunkhondo.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 10

Onani Zekariya 10:3 nkhani