2 Cema, mtengo wamlombwa, pakuti mkungudza wagwa, popeza mitengo yokoma yaipitsidwa; cemani athundu a ku Basani, pakuti nkhalango yocinjirizika yagwa pansi.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 11
Onani Zekariya 11:2 nkhani